Eksodo 37:29 BL92

29 Anapanganso mafuta opatulika akudzoza nao, ndi cofukiza coona ca pfungo lokoma, mwa macitidwe a wosanganiza.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 37

Onani Eksodo 37:29 nkhani