9 Ndipo akerubi anafunyulira mapiko ao m'mwamba, ndi kuphimba cotetezerapo ndi mao piko ao, ndi nkhope zao zopeoyana; zinapenya kucotetezerapo nkhope zao.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 37
Onani Eksodo 37:9 nkhani