Eksodo 39:15 BL92

15 Ndipo anapangira pacapacifuwa maunyolo ngati zingwe, nchito yopota ya golidi woona.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:15 nkhani