Eksodo 39:18 BL92

18 Ndi nsonga zace ziwiri zina za maunyolo awiri opotawo anazimanga pa zoikamo ziwiri, nazimanga pa zapamapewa za efodi, m'tsogolo mwace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:18 nkhani