25 Ndipo anapanga miriu ya golidi woona, napakiza miriu ndi makangaza, pa mkawo wa mwinjiro pozungulira, popakiza ndi makangaza.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 39
Onani Eksodo 39:25 nkhani