Eksodo 39:38 BL92

38 ndi guwa la nsembe lagolidi, ndi mafuta odzoza, ndi cofukiza ca pfungo lokoma, ndi nsaru yotsekera pa khomo la cihemaco;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:38 nkhani