43 Ndipo Mose anaona nchito zonse, ndipo, taonani, adaicita monga Yehova adamuuza, momwemo adacita. Ndipo Mose anawadalitsa.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 39
Onani Eksodo 39:43 nkhani