25 Koma Zipora anatenga mpeni wamwala, nadula khungu la mwana wace, naliponya pa mapazi ace; nati, Pakuti iwe ndiwe mkwati wanga wamwazi. Ndipo iye anamleka.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 4
Onani Eksodo 4:25 nkhani