24 Ndipo anaika coikapo nyali m'cihema cokomanako, popenyana ndi gome, pa mbali ya kumwela ya kacisi.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 40
Onani Eksodo 40:24 nkhani