9 Ndipo Mose ananena comweco ndi ana a Israyeli; koma sanamvera Mose cifukwa ca kuwawa mtima, ndi ukapolo wolemera.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 6
Onani Eksodo 6:9 nkhani