Eksodo 7:22 BL92

22 Ndipo alembi a Aigupto anacita momwemo ndi matsenga ao; koma mtima wa Farao unalimba, ndipo sanamvera iwo; monga adalankhula Yehova.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 7

Onani Eksodo 7:22 nkhani