33 Ndipo Mose anaturuka kwa Farao m'mudzi nasasatulira manja ace kwa Yehova; ndipo mabingu ndi matalala analeka, ndi mvula siinabvumbanso padziko.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 9
Onani Eksodo 9:33 nkhani