Eksodo 10:1 BL92

1 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao; pakuti ndaumitsa mtima wace, ndi mtima wa anyamata ace, kuti ndiike zizindikilo zanga izi pakati pao;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 10

Onani Eksodo 10:1 nkhani