31 Ndipo anaitana Mose ndi Aroni usiku, nati, Ukani, turukani pakati pa anthu anga, inu ndi ana a Israyeli; ndipo mukani katumikireni Yehova, monga mwanena.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 12
Onani Eksodo 12:31 nkhani