12 Si awa maowo tinalankhula nanu m'Aigupto ndi kuti, Tliekeni, kuti tigwirire nchito Aaigupto? pakuti kutumikira Aaigupto kutikomera si kufa m'cipululu ai.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 14
Onani Eksodo 14:12 nkhani