25 Ndipo anagurula njinga za magareta ao, nawayendetsa molemetsa; pamenepo Aaigupto anati, Tithawe pamaso pa Israyeli; pakuti Yehova alikuwagwirira nkhondo pa Aaigupto.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 14
Onani Eksodo 14:25 nkhani