26 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Tambasulira dzanja lako kunyanja, kuti madziwo abwerere kudzamiza Aaigupto, magareta ao, ndi apakavalo ao.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 14
Onani Eksodo 14:26 nkhani