Eksodo 14:28 BL92

28 Popeza madziwo anabwerera, namiza magareta ndi apakavalo, ndiwo nkhondo yonse ya Farao imene idalowa pambuyo pao m'nyanja; sanatsala wa iwowa ndi mmodzi yense.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14

Onani Eksodo 14:28 nkhani