Eksodo 14:7 BL92

7 napita nao magareta osankhika mazana asanu ndi limodzi, ndi magareta onse a m'Aigupto, ndi akapitao ao onse.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14

Onani Eksodo 14:7 nkhani