8 Ndipo Yehova analimbitsa mtima wa Farao, mfumu ya Aigupto, ndipo iye analondola ana a Israyeli; koma ana a Israyeli adaturuka ndi dzanja lokwezeka.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 14
Onani Eksodo 14:8 nkhani