27 Ndipo anafika pa Elimu, ndi pamenepo panali akasupe a madzi khumi ndi awiri, ndi akanjedza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamanga cigono cao pomwepo pa madziwo.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 15
Onani Eksodo 15:27 nkhani