Eksodo 16:9 BL92

9 Ndipo Mose anati kwa Aroni, Nena ndi khamu lonse la ana a Israyeli, Yandikizani pamaso pa Yehova, pakuti anamva madandaulo anu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 16

Onani Eksodo 16:9 nkhani