27 Ndidzatumiza kuopsa kwanga kukutsogolere, ndipo ndidzapitikitsa anthu onse amene udzafika kwao, ndipo ndidzacita kuti adani ako onse adzakuonetsa m'mbuyo mwao.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 23
Onani Eksodo 23:27 nkhani