Eksodo 25:2 BL92

2 Lankhula ndi ana a Israyeli, kuti anditengere copereka; ulandire copereka canga kwa munthu ali yense mtima wace umfunitsa mwini.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 25

Onani Eksodo 25:2 nkhani