Eksodo 25:36 BL92

36 Mitu yao ndi mphanda zao zikhale zoturuka m'mwemo; conseci cikhale cosulika cimodzi ca golidi woona.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 25

Onani Eksodo 25:36 nkhani