Eksodo 26:1 BL92

1 Ndipo uzipanga kacisi ndi nsaru zophimba khumi, za bafuta wa thonje losansitsa, ndi thonje lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira; uombemo akerubi, nchito ya mmisiri.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 26

Onani Eksodo 26:1 nkhani