29 Ndipo Aroni azinyamula maina a ana a Israyeli pa capacifuwa ca ciweruzo pamtima pace, pakulowa iye m'malo opatulika, akhale cikumbutso pankhope pa Yehova kosalekeza.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 28
Onani Eksodo 28:29 nkhani