15 Ndipo Mose anatembenuka, natsika m'phirimo, magome awiri a mboni ali m'dzanja lace; magome olembedwa kwina ndi kwina; analembedwa mbali yina ndi inzace yomwe.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 32
Onani Eksodo 32:15 nkhani