Eksodo 32:21 BL92

21 Ndipo Mose anati kwa Aroni, Anthu awa anakucitiranji, kuti iwe watengera iwo kulakwa kwakukuru kotere?

Werengani mutu wathunthu Eksodo 32

Onani Eksodo 32:21 nkhani