28 Ndipo ana a Levi anacita monga mwa mau a Mose; ndipo adagwa tsiku lija anthu ngati zikwi zitatu.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 32
Onani Eksodo 32:28 nkhani