29 Popeza Mose adati, Mdzazireni Yehova manja anu lero, pakuti yense akhale mdani wa mwana wace wamwamuna, ndi mdani wa mbale wace; kuti akudalitseni lero lino.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 32
Onani Eksodo 32:29 nkhani