Eksodo 32:30 BL92

30 Ndipo kunali m'mawa mwace, kuti Mose anati kwa anthu, Mwacimwa kucimwa kwakukulu; koma ndikwera kwa Yehova tsopano, kapena ndidzacita cotetezera ucimo wanu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 32

Onani Eksodo 32:30 nkhani