31 Ndipo Mose anabwerera kumka kwa Yehova, nati, Ha! pepani, anthu awa anacimwa kucimwa kwakukuru, nadzipangira milungu yagolidi.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 32
Onani Eksodo 32:31 nkhani