5 Pakuciona Aroni, anamanga guwa la nsembe patsogolo pace; ndipo Aroni anapfuula nati, Mawa aliko madyerero a Yehova.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 32
Onani Eksodo 32:5 nkhani