6 Ndipo Yehova anapita pamaso pace, napfuula, Yehova, Yehova, Mulungu wacifundo ndi wacisomo, wolekereza, ndi wa ukoma mtima wocuruka, ndi wacoonadi;
Werengani mutu wathunthu Eksodo 34
Onani Eksodo 34:6 nkhani