12 Anaika magango makumi asanu pa nsaru imodzi, naikanso magango makumi asanu m'mphepete mwace mwa nsaru ya cilumikizano cina; magango anakomanizana lina ndi linzace.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 36
Onani Eksodo 36:12 nkhani