Eksodo 36:29 BL92

29 Ndipo anaphatikizika pamodzi patsinde, naphatikizilca pamodzi pamutu pace ndi mphete imodzi; anatero nao onse awiri pa ngondya ziwiri.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:29 nkhani