Eksodo 36:30 BL92

30 Ndipo panali matabwa asanu ndi atatu ndi makamwa ao asiliva, makamwa khumi kudza asanu ndi limodzi; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:30 nkhani