6 Ndipo anakonza miyala yasohamu, yogwirika m'zoikamo zagolidi, yoloca ngati malocedwe a cosindikizira, ndi maina a ana a lsrayeli.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 39
Onani Eksodo 39:6 nkhani