7 Ndipo anaiika pa zapamapewa za efodi, ikhale miyala ya cikumbutso kwa ana a Israyeli; monga Yehova adamuuza Mose.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 39
Onani Eksodo 39:7 nkhani