8 Ndipo anaomba capacifuwa, nchito ya mmisiri, monga maombedwe ace a efodi; ca golidi, lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 39
Onani Eksodo 39:8 nkhani