1 Ndipo Mose anayankha nati, Koma taonani, sadzakhulupirira ine, kapena kumvera mau anga; pakuti adzanena, Yehova sanakuonekera iwe.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 4
Onani Eksodo 4:1 nkhani