15 Muka kwa Farao m'mawa; taona, aturuka kumka kumadzi; nuime kumlinda m'mbali mwa nyanja; ndi ndodo idasanduka njokayo uigwire m'dzanja lako.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 7
Onani Eksodo 7:15 nkhani