Eksodo 7:16 BL92

16 Ndipo ukanena naye, Yehova, Mulungu wa Ahebri anandituma kwa inu, ndi kuti, Lola anthu anga amuke kuti anditumukire m'cipululu; koma, taona, sunamvera ndi pano.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 7

Onani Eksodo 7:16 nkhani