Eksodo 7:17 BL92

17 Atero Yehova, Ndi ici udzadziwa kuti Ine ndine Yehova: taonani, ndidzapanda madzi ali m'nyanja ndi ndodo iri m'dzanja langa, ndipo adzasanduka mwazi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 7

Onani Eksodo 7:17 nkhani