Eksodo 36:10 BL92

10 Ndipo analumikiza nsaru zisanu yina ndi inzace; nalumikiza nsaru zisanu zina yina ndi inzace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:10 nkhani