Numeri 1:45 BL92

45 Potero owerengedwa onse a ana a Israyeli monga mwa nyumba za makolo ao, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akuturukira kunkhondo m'Israyeli;

Werengani mutu wathunthu Numeri 1

Onani Numeri 1:45 nkhani