Numeri 11:19 BL92

19 Simudzadya tsiku limodzi, kapena masiku awiri, kapena masiku asanu, kapena masiku khumi, kapena masiku makumi awiri;

Werengani mutu wathunthu Numeri 11

Onani Numeri 11:19 nkhani