24 Ndipo Mose anaturuka, nauza anthu mau a Yehova; nasonkhanitsa akuru a anthu makumi asanu ndi awiri, nawaimika pozungulira pa cihema.
Werengani mutu wathunthu Numeri 11
Onani Numeri 11:24 nkhani