Numeri 11:33 BL92

33 Nyamayi ikali pakati pa mano, asanaitafune, Mulungu anapsa mtima pa anthuwa, ndipo Yehova anawakantha anthu ndi kukantha kwakukuru ndithu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 11

Onani Numeri 11:33 nkhani